Kupeza Choonadi

Kulengedwa kwa Khristu
Phunziro 1: CHILENGEDWE: Mulungu alenga kumwamba ndi dziko lapansi
(Genesis 1:1-25)
Phunziro 2: CHILENGEDWE: Mulungu alenga munthu
(Genesis 2:4-24)
Phunziro 3: KUCHIMWA KWA MUNTHU: Kuchimwa koyamba ndi chilango chake
(Genesis 3:1-24)
Phunziro 4: KUCHIMWA KWA MUNTHU: Chigumula cha Nowa
(Genesis 6:1-9:17)
Phunziro 5: CHIWOMBOLO: Mulungu apangana ndi Abrahamu
(Genesis 12:1-8, 15:1-6)
Phunziro 6: CHIWOMBOLO: Abrahamu apeleka msembe
(Genesis 22:1-19)
Phunziro 7: CHIWOMBOLO: lonjezo la pasaka
(Eksodo 12:1-28)
Phunziro 8: CHIWOMBOLO: Malamulo khumi a Mulungu
(Eksodo 20:1-21)
Phunziro 9: CHIWOMBOLO: Lamulo lakupereka nsembe
(Levitiko 4:1-35)
Phunziro 10: KUPEMBEZA: Kutamanda Yehova m'busa wathu
(Masalimo 23: 1-6)
Phunziro 11: CHIWOMBOLO: Masomphenya a chisautso ndi ulemelero wa mtumiki wa Yehova
(Yeseya 53)
Phunziro 12: CHIWOMBOLO: Kubadwa kwa Yesu khristu
(Luka 1:26-38, 2:1-20)
Phunziro 13: CHIWOMBOLO: Ubatizo wa Yesu khristu
(Mateyu 3; Yohane 1:29-34)
Phunziro 14: CHIWOMBOLO: Kuyesedwa kwa Yesu khristu
(Mateyu 4:1-11)
Phunziro 15: CHIWOMBOLO: Yesu ayimitsa namondwe
(Maliko 4:35-41)
Phunziro 16: CHIWOMBOLO: Yesu atulutsa ziwanda
(Maliko 5:1-20)
Phunziro 17: CHIWOMBOLO: Yesu achulukitsa mikate
(Yohane 6:1-37)
Phunziro 18: CHIWOMBOLO: Yesu achiritsa odwala ndikukhululukira machimo
(Luka 5:17-26)
Phunziro 19: CHIWOMBOLO: Yesu ndi asamaliya
(Yohane 4:1-26, 39-42)
Phunziro 20: CHIWOMBOLO: Yesu aphunzitsa za njira ya Mulungu
(Luke 10:25-37; 15:11-32)
Phunziro 21: CHIWOMBOLO: Yesu aphunzitsa kupemphera
(Luka 18:9-14; Yohane 16:24)
Phunziro 22: CHIWOMBOLO: Yesu aphunzitsa zachifundo,kupemphera ndi kusala kudya
(Mateyu 6:1-34)
Phunziro 23: CHIWOMBOLO: Yesu aukitsa wakufa
(Yohane 11:1-44)
Phunziro 24: CHIWOMBOLO: Yesu aphunzitsa za wankulu mu ufumu wa Mulungu
(Mateyu 20:20-28)
Phunziro 25: CHIWOMBOLO: Mgonero wa Ambuye ndi kulosera za imfa ya Yesu
(Mateyu 26:26-30)
Phunziro 26: CHIWOMBOLO: Kupelekedwa ndi kuweluzidwa kwa Yesu
(Yohane 18:1-40 19:16)
Phunziro 27: CHIWOMBOLO: Yesu apachikidwa pa mtanda
(Luka 23:32-56)
Phunziro 28: CHIWOMBOLO: Yesu agonjetsa imfa
(Luka 24:1-35)
Phunziro 29: CHIWOMBOLO: Yesu azionetsera kwa ophunzira,nakwera kumwamba
(Luka 24:36-53)
Phunziro 30: KUWOMBA NKOTA: Kodi mufuna kusatira mawu a Mulungu?
(Yohane 3:1-21; Mateyu 7:13-14)


Get it on Google Play
Download on the App Store

Get Discovery Bible Studies on your phone

Discover copyright ©2015-2025 discoverapp.org

Chichewa scriptures from Biblica® Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero™. Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc. All rights reserved